Publicado 2 meses hace en Rap

ENCriss-IweyoProd.Real-P-x-Nomanrohy-x-Rolkhez

  • 24
  • 2
  • 0
  • 1
  • 0
  • 0
  • 1

Iweyo is love song and it is in Afro genre

#

Letra

iweyo
intro
ndiweeeeyo yoooooooo mmmh
its Encriss

verse 1

iwe ndimmodzi amene ndimakonda sindingakane sindinganamee, kukhala opanda iwe mtima mwanga nsanje mdziko langa lachikondi opanda iweeyo sizingayenda ndimabalalika , ndimabalalikaaaa or mtendere umasowa zachikondi ndimatuluka ndimafuna lady ndizikuonaniiii

Hook (Chorus)

ikakhala nkhani ya banja ndimanga ndiweyo ,
ikakhala nkhani ya ring uvale ndiweyo
ndiweyo * 2
ikakhala nkhani ya ukwati ndimanga ndiweyooooo

verse 2


I promise ndizakukonda mpka mzamera imvi ine ndikhale Adam iwe ukhale Eve nkhani yanga siyapatali ndimakukonda lady ooooh ndiwe wanga baib biab ..
undikonde mpaka Mandaaa ahaaah



Bridge
ndiwe wanga ndiweyo*2
lady ndiweyoooooooo
baib ndiweyo wanga ndiweyo *2 ndiweyoooo

Chaka chino ukwati ndimanga ndiweyo baib ukukomesa zonsezi ndiweyoo chikondi chathu bebesa ndiweyo sindingafuneso winaaa

::
/ ::

Cola

Claro